Aefeso 3:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Zinakhala choncho kuti kudzera mumpingo,+ maboma ndi maulamuliro amene ali mʼmalo akumwamba tsopano adziwe mbali zosiyanasiyana za nzeru za Mulungu.+ Aefeso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:10 Nsanja ya Olonda,11/1/2007, tsa. 295/15/1986, ptsa. 7-9
10 Zinakhala choncho kuti kudzera mumpingo,+ maboma ndi maulamuliro amene ali mʼmalo akumwamba tsopano adziwe mbali zosiyanasiyana za nzeru za Mulungu.+