Aefeso 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Choncho ndikukupemphani kuti musafooke poona mavuto amene ndikukumana nawo chifukwa cha inu, popeza mavuto amene ndikukumana nawowa achititsa kuti mulandire ulemerero.+ Aefeso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:13 Nsanja ya Olonda,2/15/2013, tsa. 28
13 Choncho ndikukupemphani kuti musafooke poona mavuto amene ndikukumana nawo chifukwa cha inu, popeza mavuto amene ndikukumana nawowa achititsa kuti mulandire ulemerero.+