Aefeso 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndikupempha kuti Mulungu amene ali ndi ulemerero waukulu, akuloleni kuti munthu wanu wamkati akhale wamphamvu,+ pogwiritsa ntchito mphamvu imene mzimu wake umapereka.
16 Ndikupempha kuti Mulungu amene ali ndi ulemerero waukulu, akuloleni kuti munthu wanu wamkati akhale wamphamvu,+ pogwiritsa ntchito mphamvu imene mzimu wake umapereka.