Aefeso 4:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 nʼcholinga choti athandize* oyerawo kuti aziyenda mʼnjira yoyenera, kuti azigwira ntchito yotumikira ena komanso kuti amange mpingo umene uli ngati thupi la Khristu,+ Aefeso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:12 Nsanja ya Olonda,6/1/1999, ptsa. 11-12
12 nʼcholinga choti athandize* oyerawo kuti aziyenda mʼnjira yoyenera, kuti azigwira ntchito yotumikira ena komanso kuti amange mpingo umene uli ngati thupi la Khristu,+