Aefeso 4:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma tizilankhula zoona ndiponso kusonyeza chikondi. Tikatero tidzakhala achikulire mʼzinthu zonse ndipo tidzatha kuchita zinthu mogwirizana ndi Khristu, amene ndi mutu.+ Aefeso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:15 Nsanja ya Olonda,6/1/1999, tsa. 15
15 Koma tizilankhula zoona ndiponso kusonyeza chikondi. Tikatero tidzakhala achikulire mʼzinthu zonse ndipo tidzatha kuchita zinthu mogwirizana ndi Khristu, amene ndi mutu.+