16 Tili ngati thupi,+ ndipo chifukwa cha iye, ziwalo zonse za thupi limeneli ndi zolumikizana bwino ndipo zimathandiza thupilo kuti lizigwira bwino ntchito. Chiwalo chilichonse cha thupili chikamagwira ntchito yake, thupili limakula bwino ndipo tidzapitiriza kukondana.+