Aefeso 4:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Choncho ndikunena komanso kuchitira umboni mwa Ambuye, kuti musapitirize kuyenda ngati mmene anthu a mitundu ina amayendera,+ potsatira maganizo awo opanda pake.+ Aefeso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:17 Nsanja ya Olonda,3/1/1993, ptsa. 8-10
17 Choncho ndikunena komanso kuchitira umboni mwa Ambuye, kuti musapitirize kuyenda ngati mmene anthu a mitundu ina amayendera,+ potsatira maganizo awo opanda pake.+