-
Aefeso 4:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Iwo ali mumdima wa maganizo ndipo ndi otalikirana ndi moyo umene umachokera kwa Mulungu, chifukwa cha umbuli umene uli mwa iwo komanso chifukwa cha kuuma kwa mitima yawo.
-