Aefeso 4:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Popeza iwo sakuthanso kuzindikira makhalidwe abwino, anadzipereka okha ku khalidwe lopanda manyazi*+ kuti achite zonyansa zamtundu uliwonse mwadyera. Aefeso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:19 Nsanja ya Olonda,5/15/2009, tsa. 127/15/2006, ptsa. 30-313/1/1993, ptsa. 12-13
19 Popeza iwo sakuthanso kuzindikira makhalidwe abwino, anadzipereka okha ku khalidwe lopanda manyazi*+ kuti achite zonyansa zamtundu uliwonse mwadyera.