Aefeso 5:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Nkhani zachiwerewere* komanso chonyansa chamtundu uliwonse kapena umbombo zisatchulidwe nʼkomwe pakati panu,+ chifukwa anthu oyera sayenera kuchita zimenezi.+ Aefeso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:3 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo, Nsanja ya Olonda,8/1/1993, tsa. 1111/1/1989, ptsa. 14-15
3 Nkhani zachiwerewere* komanso chonyansa chamtundu uliwonse kapena umbombo zisatchulidwe nʼkomwe pakati panu,+ chifukwa anthu oyera sayenera kuchita zimenezi.+