Aefeso 5:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndiponso musamaledzere ndi vinyo+ chifukwa kuledzera kungachititse kuti muchite zinthu zoipa kwambiri, koma pitirizani kudzazidwa ndi mzimu. Aefeso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:18 Nsanja ya Olonda,4/15/2011, ptsa. 20-21
18 Ndiponso musamaledzere ndi vinyo+ chifukwa kuledzera kungachititse kuti muchite zinthu zoipa kwambiri, koma pitirizani kudzazidwa ndi mzimu.