Aefeso 5:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Muziimbira limodzi masalimo, nyimbo zotamanda Mulungu ndiponso nyimbo zauzimu.+ Muziimba nyimbo+ zotamanda Yehova* mʼmitima yanu.+ Aefeso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:19 Nsanja ya Olonda,4/15/2011, ptsa. 20-215/1/1994, ptsa. 11-12
19 Muziimbira limodzi masalimo, nyimbo zotamanda Mulungu ndiponso nyimbo zauzimu.+ Muziimba nyimbo+ zotamanda Yehova* mʼmitima yanu.+