Aefeso 6:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Muzitumikira ambuye anu modzipereka, ngati mukutumikira Yehova*+ osati anthu,