Aefeso 6:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 umene ndine kazembe+ wake womangidwa ndi unyolo ndiponso kuti ndilankhule za uthengawo molimba mtima ngati mmene ndikuyenera kuchitira.
20 umene ndine kazembe+ wake womangidwa ndi unyolo ndiponso kuti ndilankhule za uthengawo molimba mtima ngati mmene ndikuyenera kuchitira.