Afilipi 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Chifukwa sindikukayikira kuti amene anayambitsa ntchito yabwino kwa inu, adzaipitiriza nʼkuimalizitsa+ mpaka tsiku la Khristu Yesu.+
6 Chifukwa sindikukayikira kuti amene anayambitsa ntchito yabwino kwa inu, adzaipitiriza nʼkuimalizitsa+ mpaka tsiku la Khristu Yesu.+