-
Afilipi 1:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Ndipo abale ambiri amene akutumikira Ambuye alimba mtima chifukwa cha kumangidwa kwanga, komanso akupitiriza kusonyeza kulimba mtima polankhula mawu a Mulungu mopanda mantha.
-