-
Afilipi 1:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Koma oyambawo akuchita zimenezo chifukwa cha mtima wokonda mikangano, osati ndi cholinga chabwino. Iwo akungofuna kundiyambitsira mavuto mʼndende muno.
-