-
Afilipi 1:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Ndiye kodi zotsatira zake nʼzotani? Ndi zoti uthenga wokhudza Khristu ukufalitsidwabe, kaya ndi mwachiphamaso kapena mʼchoonadi ndipo ine ndikusangalala chifukwa cha zimenezi. Ndipotu ndipitirizabe kusangalala
-