-
Afilipi 1:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Tsopano ngati ndipitirizabe kukhala ndi moyo mʼthupi limene ndili naloli, ntchito ya manja anga idzawonjezeka, koma choti ndisankhe pamenepa sindinena.
-