Afilipi 1:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndagwira njakata kuti ndisankhe chiti pa zinthu ziwirizi, chifukwa ndikulakalaka nditamasulidwa nʼkukakhala ndi Khristu,+ zimene kunena zoona ndi zabwino kwambiri.+ Afilipi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:23 Nsanja ya Olonda,8/15/2008, tsa. 283/1/1995, ptsa. 30-31
23 Ndagwira njakata kuti ndisankhe chiti pa zinthu ziwirizi, chifukwa ndikulakalaka nditamasulidwa nʼkukakhala ndi Khristu,+ zimene kunena zoona ndi zabwino kwambiri.+