Afilipi 1:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Komanso simukuchita mantha mʼnjira iliyonse ndi amene akukutsutsani. Umenewu ndi umboni wakuti adzawonongedwa,+ koma kwa inu, ndi umboni wakuti mudzapulumutsidwa+ ndipo umboni umenewu ndi wochokera kwa Mulungu.
28 Komanso simukuchita mantha mʼnjira iliyonse ndi amene akukutsutsani. Umenewu ndi umboni wakuti adzawonongedwa,+ koma kwa inu, ndi umboni wakuti mudzapulumutsidwa+ ndipo umboni umenewu ndi wochokera kwa Mulungu.