Afilipi 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Muzichita zonse zimene mungathe kuti muzilimbikitsana mwa Khristu, muzitonthozana mwachikondi, muzisonyeza mzimu wokonda kuchitira zinthu limodzi,* muzisonyezana chikondi chachikulu komanso chifundo. Afilipi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:1 Nsanja ya Olonda,1/15/1986, tsa. 18
2 Muzichita zonse zimene mungathe kuti muzilimbikitsana mwa Khristu, muzitonthozana mwachikondi, muzisonyeza mzimu wokonda kuchitira zinthu limodzi,* muzisonyezana chikondi chachikulu komanso chifundo.