-
Afilipi 2:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Abale ndi alongo anga okondedwa, pamene ndinali nanu limodzi, nthawi zonse munkamvera. Simunachite zimenezi pa nthawi yokhayo imene ine ndinalipo koma ngakhale panopa pamene sindilinso ndi inu, mukumvera kwambiri. Mofanana ndi zimenezi, aliyense wa inu apitirize kuyesetsa kuchita zimenezi mwamantha ndi kunjenjemera kuti adzapulumuke.
-