-
Afilipi 2:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Chifukwa Mulungu ndi amene amakulimbitsani. Amakupatsani mtima wofuna kuchita zinthu zimene iye amakonda komanso mphamvu zochitira zinthuzo. Iye amachita zimenezi chifukwa ndi zimene zimamusangalatsa.
-