Afilipi 2:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pamene mukuchita zimenezi, mugwire mwamphamvu mawu amoyo.+ Mukatero ndidzakhala ndi chifukwa chosangalalira mʼtsiku la Khristu, chifukwa ndidzadziwa kuti sindinathamange pachabe kapena kuchita khama pachabe.
16 Pamene mukuchita zimenezi, mugwire mwamphamvu mawu amoyo.+ Mukatero ndidzakhala ndi chifukwa chosangalalira mʼtsiku la Khristu, chifukwa ndidzadziwa kuti sindinathamange pachabe kapena kuchita khama pachabe.