Afilipi 2:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Koma inu mukudziwa chitsanzo chabwino chimene Timoteyo anasonyeza, kuti monga mwana+ ndi bambo ake, watumikira ngati kapolo limodzi ndi ine pofalitsa uthenga wabwino. Afilipi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:22 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),4/2018, tsa. 14
22 Koma inu mukudziwa chitsanzo chabwino chimene Timoteyo anasonyeza, kuti monga mwana+ ndi bambo ake, watumikira ngati kapolo limodzi ndi ine pofalitsa uthenga wabwino.