-
Afilipi 2:27Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
27 Nʼzoona kuti anadwaladi mpaka kutsala pangʼono kufa. Koma Mulungu anamuchitira chifundo. Ndipotu chifundo chimenecho sanachitire iye yekha, koma anachitiranso ine kuti chisoni changa chisawonjezeke.
-