Afilipi 2:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Ndiye monga mwa nthawi zonse, mulandireni ndi manja awiri ngati mmene mumachitira polandira otsatira a Ambuye. Mumulandire mwachimwemwe ndipo abale ngati amenewa muziwalemekeza kwambiri,+ Afilipi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:29 Nsanja ya Olonda,10/1/1988, ptsa. 15-20
29 Ndiye monga mwa nthawi zonse, mulandireni ndi manja awiri ngati mmene mumachitira polandira otsatira a Ambuye. Mumulandire mwachimwemwe ndipo abale ngati amenewa muziwalemekeza kwambiri,+