Afilipi 2:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 chifukwa anatsala pangʼono kufa pamene ankagwira ntchito ya Khristu* ndipo anaika moyo wake pachiswe* kuti adzanditumikire mʼmalo mwa inu, popeza simukanatha kubwera kuno kuti mudzandithandize.+ Afilipi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:30 Nsanja ya Olonda,8/15/1996, ptsa. 28-29
30 chifukwa anatsala pangʼono kufa pamene ankagwira ntchito ya Khristu* ndipo anaika moyo wake pachiswe* kuti adzanditumikire mʼmalo mwa inu, popeza simukanatha kubwera kuno kuti mudzandithandize.+