Afilipi 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pomalizira abale anga, pitirizani kusangalala monga otsatira a Ambuye.+ Kubwereza kulemba zinthu zimene ndinakulemberani kale si vuto kwa ine, koma ndi chitetezo kwa inu.
3 Pomalizira abale anga, pitirizani kusangalala monga otsatira a Ambuye.+ Kubwereza kulemba zinthu zimene ndinakulemberani kale si vuto kwa ine, koma ndi chitetezo kwa inu.