Afilipi 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Chifukwa ife tinachita mdulidwe weniweni,+ ife amene tikuchita utumiki wopatulika motsogoleredwa ndi mzimu wa Mulungu. Timadzitamandira mwa Khristu Yesu+ ndipo sitidalira zinthu zimene anthu amaziona kuti ndi zofunika,
3 Chifukwa ife tinachita mdulidwe weniweni,+ ife amene tikuchita utumiki wopatulika motsogoleredwa ndi mzimu wa Mulungu. Timadzitamandira mwa Khristu Yesu+ ndipo sitidalira zinthu zimene anthu amaziona kuti ndi zofunika,