-
Afilipi 3:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 ngakhale kuti ineyo, kuposa wina aliyense, ndili ndi zifukwa zodalira zinthu zimene anthu amaziona kuti ndi zofunika.
Ngati pali munthu wina amene akuganiza kuti ali ndi zifukwa zodalira zinthu zimene anthu amaziona kuti ndi zofunika, ine ndikuposa ameneyo, chifukwa:
-