Afilipi 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kunena za kudzipereka, ndinkazunza mpingo.+ Kunena zochita chilungamo potsatira chilamulo, ndinasonyeza kuti ndilibe chifukwa chondinenezera. Afilipi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:6 Nsanja ya Olonda,6/15/1999, ptsa. 29-31
6 Kunena za kudzipereka, ndinkazunza mpingo.+ Kunena zochita chilungamo potsatira chilamulo, ndinasonyeza kuti ndilibe chifukwa chondinenezera.