Afilipi 3:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Chifukwa pali anthu ambiri amene akuchita zinthu ngati adani a mtengo wozunzikirapo* wa Khristu. Kale ndinkawatchula pafupipafupi koma pano ndimawatchula ndikugwetsa misozi.
18 Chifukwa pali anthu ambiri amene akuchita zinthu ngati adani a mtengo wozunzikirapo* wa Khristu. Kale ndinkawatchula pafupipafupi koma pano ndimawatchula ndikugwetsa misozi.