Afilipi 3:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Koma ife ndife nzika+ zakumwamba+ ndipo tikuyembekezera mwachidwi mpulumutsi wochokera kumeneko amene ndi Ambuye Yesu Khristu.+ Afilipi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:20 Nsanja ya Olonda,8/15/2012, tsa. 11
20 Koma ife ndife nzika+ zakumwamba+ ndipo tikuyembekezera mwachidwi mpulumutsi wochokera kumeneko amene ndi Ambuye Yesu Khristu.+