Afilipi 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Choncho inu abale anga amene ndimakukondani ndipo ndikulakalaka kukuonani, ndinu chimwemwe changa ndi chipewa changa chaulemerero.+ Okondedwa anga, ndikukulimbikitsani kuti mupitirize kukhala okhulupirika+ kwa Ambuye.
4 Choncho inu abale anga amene ndimakukondani ndipo ndikulakalaka kukuonani, ndinu chimwemwe changa ndi chipewa changa chaulemerero.+ Okondedwa anga, ndikukulimbikitsani kuti mupitirize kukhala okhulupirika+ kwa Ambuye.