Afilipi 4:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ine ndikusangalala kwambiri mwa Ambuye kuti tsopano mwayambiranso kundiganizira.+ Ndikudziwa kuti mwakhala mukundiganizira nthawi yonseyi, koma kungoti mumasowa mpata wosonyeza zimenezi.
10 Ine ndikusangalala kwambiri mwa Ambuye kuti tsopano mwayambiranso kundiganizira.+ Ndikudziwa kuti mwakhala mukundiganizira nthawi yonseyi, koma kungoti mumasowa mpata wosonyeza zimenezi.