-
Afilipi 4:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Chifukwa pamene ndinali ku Tesalonika, inu munanditumizira kenakake kuti kandithandize pa zimene ndinkafunikira ndipo simunachite zimenezi kamodzi kokha, koma kawiri.
-