Akolose 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 chifukwa cha chiyembekezo chodzalandira zinthu zimene akusungirani kumwamba.+ Munamva za chiyembekezo chimenechi mʼmbuyomu pamene munamva uthenga wa choonadi, womwe ndi uthenga wabwino
5 chifukwa cha chiyembekezo chodzalandira zinthu zimene akusungirani kumwamba.+ Munamva za chiyembekezo chimenechi mʼmbuyomu pamene munamva uthenga wa choonadi, womwe ndi uthenga wabwino