Akolose 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Zimenezi ndi zimene munaphunzira kwa Epafura,+ kapolo mnzathu wokondedwa, amene ndi mtumiki wokhulupirika wa Khristu mʼmalo mwa ife. Akolose Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:7 Nsanja ya Olonda,5/15/1997, ptsa. 30-31
7 Zimenezi ndi zimene munaphunzira kwa Epafura,+ kapolo mnzathu wokondedwa, amene ndi mtumiki wokhulupirika wa Khristu mʼmalo mwa ife.