Akolose 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iye ndi amenenso anatidziwitsa za chikondi chanu chimene munachisonyeza mothandizidwa ndi mzimu wa Mulungu.*
8 Iye ndi amenenso anatidziwitsa za chikondi chanu chimene munachisonyeza mothandizidwa ndi mzimu wa Mulungu.*