Akolose 1:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndiponso iye analipo kale zinthu zina zonse zisanakhaleko+ ndipo zinthu zina zonse zinakhalapo kudzera mwa iye.
17 Ndiponso iye analipo kale zinthu zina zonse zisanakhaleko+ ndipo zinthu zina zonse zinakhalapo kudzera mwa iye.