Akolose 1:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Iye ndi mutu wa thupi, lomwe ndi mpingo.+ Iye ndi chiyambi, woyamba kubadwa kuchokera kwa akufa,+ kuti adzakhale woyamba pa zinthu zonse. Akolose Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:18 Nsanja ya Olonda,4/1/2007, tsa. 22
18 Iye ndi mutu wa thupi, lomwe ndi mpingo.+ Iye ndi chiyambi, woyamba kubadwa kuchokera kwa akufa,+ kuti adzakhale woyamba pa zinthu zonse.