Akolose 1:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Zili choncho chifukwa chakuti Mulungu zinamusangalatsa kuti makhalidwe ake onse akhale mwa Khristu.+ Akolose Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:19 Nsanja ya Olonda,8/15/2011, tsa. 24
19 Zili choncho chifukwa chakuti Mulungu zinamusangalatsa kuti makhalidwe ake onse akhale mwa Khristu.+