Akolose 1:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 tsopano wagwirizana nanunso kudzera mu imfa ya mwana wake amene anapereka thupi lake lanyama nʼcholinga choti akuperekeni pamaso pa Mulunguyo, muli opatulika ndi opanda chilema ndiponso opanda chifukwa chokunenezerani.+ Akolose Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:22 Nsanja ya Olonda,12/15/1994, tsa. 12
22 tsopano wagwirizana nanunso kudzera mu imfa ya mwana wake amene anapereka thupi lake lanyama nʼcholinga choti akuperekeni pamaso pa Mulunguyo, muli opatulika ndi opanda chilema ndiponso opanda chifukwa chokunenezerani.+