-
Akolose 1:27Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
27 Mulungu zinamusangalatsa kuululira oyera pakati pa anthu a mitundu ina chinsinsi chopatulikachi,+ chomwe chili ndi ulemerero wochuluka komanso chuma chauzimu. Chinsinsi chimenechi ndi Khristu amene ndi wogwirizana ndi inuyo, kutanthauza kuti muli ndi chiyembekezo chodzalandira ulemerero limodzi ndi Khristuyo.+
-