Akolose 1:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Tikulengeza, kuchenjeza ndi kuphunzitsa munthu aliyense za iyeyu mu nzeru zonse, kuti tipereke munthu aliyense kwa Mulungu ali wolimba mwauzimu mogwirizana ndi Khristu.+
28 Tikulengeza, kuchenjeza ndi kuphunzitsa munthu aliyense za iyeyu mu nzeru zonse, kuti tipereke munthu aliyense kwa Mulungu ali wolimba mwauzimu mogwirizana ndi Khristu.+