Akolose 1:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Kuti ndikwanitse kuchita zimenezi, ndikugwira ntchito mwakhama ndipo ndikuyesetsa kwambiri podalira mphamvu zake zimene zikugwira ntchito mwamphamvu mwa ine.+ Akolose Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:29 Nsanja ya Olonda,12/15/1994, tsa. 13
29 Kuti ndikwanitse kuchita zimenezi, ndikugwira ntchito mwakhama ndipo ndikuyesetsa kwambiri podalira mphamvu zake zimene zikugwira ntchito mwamphamvu mwa ine.+