Akolose 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Simukusowa kalikonse chifukwa cha iye, amene ndi mutu wa boma lililonse ndi ulamuliro uliwonse.+