Akolose 2:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Sakutsatira amene ndi mutu,+ amene kudzera mwa iye, thupi lonse limapeza zonse zimene limafunikira ndipo ziwalo zake ndi zolumikizana bwino ndi mfundo zake komanso minyewa ndipo limakulabe mothandizidwa ndi Mulungu.+ Akolose Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:19 Nsanja ya Olonda,12/15/1994, tsa. 25
19 Sakutsatira amene ndi mutu,+ amene kudzera mwa iye, thupi lonse limapeza zonse zimene limafunikira ndipo ziwalo zake ndi zolumikizana bwino ndi mfundo zake komanso minyewa ndipo limakulabe mothandizidwa ndi Mulungu.+